Yobu 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuti achititse kulira kwa wonyozeka kupita kwa iye.Choncho iye amamva kulira kwa osautsika.+ Salimo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti muweruze mwana wamasiye komanso woponderezedwa.+Mudzatero kuti munthu wamba wochokera kufumbi asachititsenso anthu ena kunjenjemera.+ Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku? Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.
18 Kuti muweruze mwana wamasiye komanso woponderezedwa.+Mudzatero kuti munthu wamba wochokera kufumbi asachititsenso anthu ena kunjenjemera.+
7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.