Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+ Levitiko 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo azipereka mbali ina ya nsembe yachiyanjanoyo monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Azipereka mafuta+ okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+ Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Tsopano lamulo la nsembe yachiyanjano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova lili motere:
3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+
3 Pamenepo azipereka mbali ina ya nsembe yachiyanjanoyo monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Azipereka mafuta+ okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+