Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Utenge mafuta+ onse okuta matumbo,+ mafuta a pachiwindi,*+ impso ziwiri ndi mafuta ake, n’kuzitentha* paguwa lansembe.+

  • Levitiko 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Musamadye mafuta+ alionse a ng’ombe, a mwana wa nkhosa, kapena a mbuzi.

  • Levitiko 7:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iye azibweretsa mafuta+ pamodzi ndi nganga monga nsembe kwa Yehova yotentha ndi moto. Azibweretsa mafutawo pamodzi ndi nganga kuti aziweyule* uku ndi uku, monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova.

  • 1 Mafumu 8:64
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 64 Tsiku limenelo, pakati pa bwalo la nyumba ya Yehova+ panayenera kupatulidwa ndi mfumu, chifukwa inafunika kuperekerapo nsembe yopsereza, nsembe yambewu, ndi mafuta a nsembe zachiyanjano. Inatero popeza guwa lansembe lamkuwa+ limene lili pamaso pa Yehova linachepa, ndipo nsembe yopsereza, nsembe yambewu, ndi mafuta+ a nsembe zachiyanjano sizikanakwanapo.

  • Ezekieli 44:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “‘Ansembe achilevi,+ ana a Zadoki,+ amene anali kugwira ntchito za pamalo anga opatulika pamene ana a Isiraeli anachoka kwa ine n’kupita kutali,+ amenewa adzandiyandikira ndi kunditumikira. Iwo adzaima pamaso panga+ ndi kundipatsa mafuta+ ndi magazi,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena