Levitiko 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo Mose anatenga mafuta onse okuta matumbo, mafuta a pachiwindi ndi impso ziwiri ndi mafuta ake, n’kuzitentha paguwa lansembe.+ Levitiko 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kunena za mafuta+ a ng’ombeyo, mchira wa mafuta+ wa nkhosa, mafuta okuta matumbo, impso ndi mafuta a pachiwindi,
16 Ndipo Mose anatenga mafuta onse okuta matumbo, mafuta a pachiwindi ndi impso ziwiri ndi mafuta ake, n’kuzitentha paguwa lansembe.+
19 Kunena za mafuta+ a ng’ombeyo, mchira wa mafuta+ wa nkhosa, mafuta okuta matumbo, impso ndi mafuta a pachiwindi,