Levitiko 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero Mose anatenga mafuta onse okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake, nʼkuziwotcha paguwa lansembe.+
16 Atatero Mose anatenga mafuta onse okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake, nʼkuziwotcha paguwa lansembe.+