Levitiko 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wansembe aziwaza magazi a nyamazo paguwa lansembe la Yehova+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako, ndipo azitentha mafuta+ ake kuti likhale fungo lokhazika mtima pansi loperekedwa kwa Yehova.+
6 Wansembe aziwaza magazi a nyamazo paguwa lansembe la Yehova+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako, ndipo azitentha mafuta+ ake kuti likhale fungo lokhazika mtima pansi loperekedwa kwa Yehova.+