Levitiko 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo wansembe azitentha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi. Mafuta onse ndi a Yehova.+ Levitiko 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno wansembe azitentha mafutawo+ paguwa lansembe, koma ngangayo izikhala ya Aroni ndi ana ake.+
16 Ndipo wansembe azitentha zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi. Mafuta onse ndi a Yehova.+
31 Ndiyeno wansembe azitentha mafutawo+ paguwa lansembe, koma ngangayo izikhala ya Aroni ndi ana ake.+