Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno wansembeyo aziphimba+ tchimo limene munthuyo wachita. Aziphimba tchimo lililonse mwa machimo amenewa, ndipo azikhululukidwa. Ufa wotsalawo uzikhala wa wansembe+ mofanana ndi nsembe yambewu.’”

  • Levitiko 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda chofufumitsa+ ndi kudya mkatewo m’malo oyera. Aziudyera m’bwalo la chihema chokumanako.

  • Levitiko 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kenako Mose anatenga nganga+ ndi kuiweyula uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+ Nganga imeneyi anaitenga pa nkhosa yowalongera unsembe ndipo inakhala gawo+ la Mose, monga mmene Yehova analamulira Mose.

  • Numeri 18:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Uzitenga nyama yake kuti ikhale yako, mofanana ndi nganga ya nsembe yoweyula, komanso mwendo wam’mbuyo wakumanja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena