Ekisodo 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kenako utenge nganga ya nkhosa yolongera Aroni unsembe,+ ndi kuiweyulira uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo ikhale gawo lako. Levitiko 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye azibweretsa mafuta+ pamodzi ndi nganga monga nsembe kwa Yehova yotentha ndi moto. Azibweretsa mafutawo pamodzi ndi nganga kuti aziweyule* uku ndi uku, monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova.
26 “Kenako utenge nganga ya nkhosa yolongera Aroni unsembe,+ ndi kuiweyulira uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo ikhale gawo lako.
30 Iye azibweretsa mafuta+ pamodzi ndi nganga monga nsembe kwa Yehova yotentha ndi moto. Azibweretsa mafutawo pamodzi ndi nganga kuti aziweyule* uku ndi uku, monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova.