Levitiko 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Mose anatenga nganga+ ndi kuiweyula uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+ Nganga imeneyi anaitenga pa nkhosa yowalongera unsembe ndipo inakhala gawo+ la Mose, monga mmene Yehova analamulira Mose. Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+
29 Kenako Mose anatenga nganga+ ndi kuiweyula uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+ Nganga imeneyi anaitenga pa nkhosa yowalongera unsembe ndipo inakhala gawo+ la Mose, monga mmene Yehova analamulira Mose.
6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+