Ekisodo 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako utenge chidale cha nkhosa yoikira+ Aroni kuti akhale wansembe ndipo uchiyendetse uku ndi uku monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo idzakhale yako.
26 Kenako utenge chidale cha nkhosa yoikira+ Aroni kuti akhale wansembe ndipo uchiyendetse uku ndi uku monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo idzakhale yako.