Ekisodo 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kenako utenge nganga ya nkhosa yolongera Aroni unsembe,+ ndi kuiweyulira uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo ikhale gawo lako.
26 “Kenako utenge nganga ya nkhosa yolongera Aroni unsembe,+ ndi kuiweyulira uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo ikhale gawo lako.