Levitiko 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Mose anatenga chidale nʼkuchiyendetsa uku ndi uku monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku yoperekedwa kwa Yehova.+ Chidale chimenechi anachitenga pa nkhosa yowaikira kuti akhale ansembe ndipo chinakhala gawo la Mose, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.+ Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali mʼgulu la ansembe ake,+Ndipo Samueli anali mʼgulu la anthu amene ankaitana pa dzina lake.+ Iwo ankaitana Yehova,Ndipo iye ankawayankha.+
29 Kenako Mose anatenga chidale nʼkuchiyendetsa uku ndi uku monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku yoperekedwa kwa Yehova.+ Chidale chimenechi anachitenga pa nkhosa yowaikira kuti akhale ansembe ndipo chinakhala gawo la Mose, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.+
6 Mose ndi Aroni anali mʼgulu la ansembe ake,+Ndipo Samueli anali mʼgulu la anthu amene ankaitana pa dzina lake.+ Iwo ankaitana Yehova,Ndipo iye ankawayankha.+