Levitiko 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Mose anatenga nganga+ ndi kuiweyula uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+ Nganga imeneyi anaitenga pa nkhosa yowalongera unsembe ndipo inakhala gawo+ la Mose, monga mmene Yehova analamulira Mose.
29 Kenako Mose anatenga nganga+ ndi kuiweyula uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+ Nganga imeneyi anaitenga pa nkhosa yowalongera unsembe ndipo inakhala gawo+ la Mose, monga mmene Yehova analamulira Mose.