Levitiko 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Musamadye mafuta+ alionse a ng’ombe, a mwana wa nkhosa, kapena a mbuzi. 1 Samueli 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wopereka nsembeyo akanena kuti: “Yembekeza kaye apsereze mafutawo,+ kenako utenge chilichonse chimene mtima wako ukufuna,”+ iye anali kuyankha kuti: “Ayi, ndipatse pompano, ukapanda kundipatsa, ndichita kulanda!”+
23 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Musamadye mafuta+ alionse a ng’ombe, a mwana wa nkhosa, kapena a mbuzi.
16 Wopereka nsembeyo akanena kuti: “Yembekeza kaye apsereze mafutawo,+ kenako utenge chilichonse chimene mtima wako ukufuna,”+ iye anali kuyankha kuti: “Ayi, ndipatse pompano, ukapanda kundipatsa, ndichita kulanda!”+