Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo ana a Dani anamuuza kuti: “Usayandikire kuno ndipo tisamvenso mawu akowo, chifukwa anthu olusa+ angakupwetekeni, ndipo iweyo ungataye moyo wako ndi kutayitsa moyo wa anthu a m’nyumba yako.”

  • Nehemiya 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Abwanamkubwa amene analipo ine ndisanakhale, ankalemetsa anthu, ndipo tsiku ndi tsiku anali kulandira masekeli* 40 a siliva kuti akagule chakudya ndi vinyo. Komanso atumiki awo anali kupondereza anthu.+ Koma ine sindinachite zimenezo+ chifukwa choopa Mulungu.+

  • Mika 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+

  • 1 Petulo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena