1 Timoteyo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+ Tito 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 N’kofunika kuwatseka pakamwa, pakuti anthu amenewa, pofuna kupeza phindu mwachinyengo,+ akuwonongabe mabanja athunthu+ mwa kuphunzitsa zinthu zimene sayenera kuphunzitsa.
2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+
11 N’kofunika kuwatseka pakamwa, pakuti anthu amenewa, pofuna kupeza phindu mwachinyengo,+ akuwonongabe mabanja athunthu+ mwa kuphunzitsa zinthu zimene sayenera kuphunzitsa.