Luka 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Onse awiriwo anali olungama+ pamaso pa Mulungu chifukwa choyenda mokhulupirika,+ mogwirizana ndi malamulo onse+ komanso zofunika za m’chilamulo+ cha Yehova.+ Aroma 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+ Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+ 1 Timoteyo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuti usunge lamulolo. Ulisunge uli wopanda banga ndi wopanda chifukwa chokunenezera, kufikira kuonekera+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.
6 Onse awiriwo anali olungama+ pamaso pa Mulungu chifukwa choyenda mokhulupirika,+ mogwirizana ndi malamulo onse+ komanso zofunika za m’chilamulo+ cha Yehova.+
19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+
14 kuti usunge lamulolo. Ulisunge uli wopanda banga ndi wopanda chifukwa chokunenezera, kufikira kuonekera+ kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.