Aroma 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kutinso adzakhale tate wa ana odulidwa, osati wa okhawo ochita mdulidwe, komanso wa amene amayenda moyenerera m’mapazi a chikhulupiriro chimene bambo wathu+ Abulahamu anali nacho asanadulidwe. Agalatiya 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngati tikukhala mwa mzimu, tiyeninso tipitirize kuyenda motsogoleredwa ndi mzimuwo.+ Afilipi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, mulimonse mmene tapitira patsogolo, tiyeni tipitirize kupita patsogolo mwa kuyenda moyenera+ m’njira yomweyo.
12 Kutinso adzakhale tate wa ana odulidwa, osati wa okhawo ochita mdulidwe, komanso wa amene amayenda moyenerera m’mapazi a chikhulupiriro chimene bambo wathu+ Abulahamu anali nacho asanadulidwe.
16 Komabe, mulimonse mmene tapitira patsogolo, tiyeni tipitirize kupita patsogolo mwa kuyenda moyenera+ m’njira yomweyo.