Aroma 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu anachita izi kuti ife amene tikuyenda motsatira za mzimu,+ osati motsatira zofuna za thupi, tikwaniritse miyezo yolungama ya Chilamulo.+
4 Mulungu anachita izi kuti ife amene tikuyenda motsatira za mzimu,+ osati motsatira zofuna za thupi, tikwaniritse miyezo yolungama ya Chilamulo.+