Agalatiya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’malomwake ndikuti, Pitirizani kuyenda mwa mzimu,+ ndipo simudzatsatira chilakolako cha thupi ngakhale pang’ono.+ Agalatiya 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komanso ngati mukutsogoleredwa ndi mzimu,+ simuli pansi pa chilamulo.+
16 M’malomwake ndikuti, Pitirizani kuyenda mwa mzimu,+ ndipo simudzatsatira chilakolako cha thupi ngakhale pang’ono.+