Aroma 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uchimo usakhale mbuye kwa inu, chifukwa simuli pansi pa chilamulo+ koma pansi pa kukoma mtima kwakukulu.+ Aroma 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti chilamulo+ cha mzimu+ umene umapatsa moyo+ mwa Khristu Yesu chakumasulani+ ku chilamulo cha uchimo ndi cha imfa.+
14 Uchimo usakhale mbuye kwa inu, chifukwa simuli pansi pa chilamulo+ koma pansi pa kukoma mtima kwakukulu.+
2 Pakuti chilamulo+ cha mzimu+ umene umapatsa moyo+ mwa Khristu Yesu chakumasulani+ ku chilamulo cha uchimo ndi cha imfa.+