Aroma 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinalitu wamoyo chilamulo chisanabwere.+ Koma pamene malamulo anafika,+ uchimo unakhalanso ndi moyo, koma ineyo ndinafa.+ 2 Akorinto 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndipo chifukwa cha iyeyo ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ ndipo ndife ogwirizana osati kudzera m’malamulo olembedwa,+ koma mu mzimu.+ Pakuti malamulo olembedwa amaweruza munthu+ kuti afe, koma mzimu umapatsa munthu moyo.+
9 Ndinalitu wamoyo chilamulo chisanabwere.+ Koma pamene malamulo anafika,+ uchimo unakhalanso ndi moyo, koma ineyo ndinafa.+
6 ndipo chifukwa cha iyeyo ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ ndipo ndife ogwirizana osati kudzera m’malamulo olembedwa,+ koma mu mzimu.+ Pakuti malamulo olembedwa amaweruza munthu+ kuti afe, koma mzimu umapatsa munthu moyo.+