1 Timoteyo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akulu otsogolera+ bwino apatsidwe ulemu waukulu,+ makamaka amene amachita khama kulankhula ndi kuphunzitsa.+ 2 Timoteyo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+ Tito 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa. Yakobo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu,+ podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chachikulu.+
17 Akulu otsogolera+ bwino apatsidwe ulemu waukulu,+ makamaka amene amachita khama kulankhula ndi kuphunzitsa.+
24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu,+ koma ayenera kukhala wodekha kwa onse.+ Ayeneranso kukhala woyenerera kuphunzitsa,+ wougwira mtima pokumana ndi zoipa,+
9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.
3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu,+ podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chachikulu.+