1 Atesalonika 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani. Aheberi 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani amene akutsogolera pakati panu.+ Amenewa anakuphunzitsani mawu a Mulungu. Ndipo pamene mukuonetsetsa zotsatira zabwino za khalidwe lawo, tsanzirani+ chikhulupiriro chawo.+
12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani.
7 Kumbukirani amene akutsogolera pakati panu.+ Amenewa anakuphunzitsani mawu a Mulungu. Ndipo pamene mukuonetsetsa zotsatira zabwino za khalidwe lawo, tsanzirani+ chikhulupiriro chawo.+