1 Akorinto 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzitsanzira ine, monga mmene inenso ndimatsanzirira Khristu.+ 2 Atesalonika 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti inuyo mukudziwa mmene muyenera kutitsanzirira.+ Sitinakhale mosalongosoka pakati panu,+