1 Akorinto 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero ndikukuchondererani, tsanzirani ineyo.+ 1 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri,
6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri,