2 Timoteyo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakati pa anthu amenewa pamachokera anthu amene amalowerera mozemba m’mabanja,+ ndi kugwira amayi osiyanasiyana kuti akhale akapolo awo. Amayiwo amakhala ofooka, olemedwa ndi machimo, ndiponso otengeka ndi zilakolako zosiyanasiyana,+
6 Pakati pa anthu amenewa pamachokera anthu amene amalowerera mozemba m’mabanja,+ ndi kugwira amayi osiyanasiyana kuti akhale akapolo awo. Amayiwo amakhala ofooka, olemedwa ndi machimo, ndiponso otengeka ndi zilakolako zosiyanasiyana,+