5 Zimayambitsanso mapokoso achiwawa pa zinthu zazing’ono pakati pa anthu opotoka maganizo+ ndi osadziwa choonadi,+ poganiza kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi njira yopezera phindu.+
2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.