2 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+ 2 Timoteyo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano monga mmene Yane ndi Yambure+ anatsutsira Mose, anthu amenewanso akupitiriza kutsutsa choonadi.+ Iwo ali ndi maganizo opotoka kwambiri,+ ndipo sakuyenerera chikhulupirirochi.+ Yuda 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+
3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+
8 Tsopano monga mmene Yane ndi Yambure+ anatsutsira Mose, anthu amenewanso akupitiriza kutsutsa choonadi.+ Iwo ali ndi maganizo opotoka kwambiri,+ ndipo sakuyenerera chikhulupirirochi.+
10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+