Afilipi 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti alipo ambiri amene ndinali kuwatchula kawirikawiri, koma tsopano ndikuwatchula ndi misozi, amene akuyenda monga adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu.+ 2 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzasiya kumvetsera choonadi, n’kutembenukira ku nkhani zonama.+ Tito 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asamasamale nthano zachiyuda+ ndi malamulo a anthu+ amene asiya choonadi.+
18 Pakuti alipo ambiri amene ndinali kuwatchula kawirikawiri, koma tsopano ndikuwatchula ndi misozi, amene akuyenda monga adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu.+