1 Samueli 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthuyo akanena kuti: “Yembekeza kaye apsereze mafutawo+ kenako utenge chilichonse chimene ukufuna,” iye ankayankha kuti: “Ayi, ndipatse pompano, apo ayi ndichita kulanda!”
16 Munthuyo akanena kuti: “Yembekeza kaye apsereze mafutawo+ kenako utenge chilichonse chimene ukufuna,” iye ankayankha kuti: “Ayi, ndipatse pompano, apo ayi ndichita kulanda!”