Levitiko 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wansembe aziwaza magazi a nyamazo paguwa lansembe la Yehova limene lili pakhomo la chihema chokumanako, ndipo aziwotcha mafuta ake kuti likhale kafungo kosangalatsa* kwa Yehova.+
6 Wansembe aziwaza magazi a nyamazo paguwa lansembe la Yehova limene lili pakhomo la chihema chokumanako, ndipo aziwotcha mafuta ake kuti likhale kafungo kosangalatsa* kwa Yehova.+