8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+
19 “‘Ansembe achilevi+ omwe ndi ana a Zadoki,+ amene amayandikira kwa ine ndi kunditumikira,+ uwapatse ng’ombe yaing’ono yamphongo kuchokera pagulu la ziweto kuti ikhale nsembe yamachimo.’+ Watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.