Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+

      Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+

      Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+

  • Oweruza 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Gidiyoni anawayankha kuti: “Ineyo sindikhala wokulamulirani, ngakhalenso mwana wanga sakhala wokulamulirani.+ Yehova ndiye azikulamulirani.”+

  • 1 Samueli 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+

  • Salimo 74:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+

      Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+

  • Yesaya 33:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena