Oweruza 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Gidiyoni anawayankha kuti: “Ineyo sindikhala wokulamulirani, ngakhalenso mwana wanga sakhala wokulamulirani. Yehova ndi amene azikulamulirani.”+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:23 Nsanja ya Olonda,3/1/1987, tsa. 9
23 Koma Gidiyoni anawayankha kuti: “Ineyo sindikhala wokulamulirani, ngakhalenso mwana wanga sakhala wokulamulirani. Yehova ndi amene azikulamulirani.”+