Ekisodo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.+ 1 Samueli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani mʼmasautso anu onse ndiponso mʼmavuto anu, ndipo munanena kuti: “Ayi, mutisankhire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova potengera mafuko anu ndiponso mabanja anu.’”* Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+ Yesaya 43:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndine Yehova, Woyera wanu,+ Mlengi wa Isiraeli+ ndiponso Mfumu yanu.”+
19 Koma lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani mʼmasautso anu onse ndiponso mʼmavuto anu, ndipo munanena kuti: “Ayi, mutisankhire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova potengera mafuko anu ndiponso mabanja anu.’”*
22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+