Oweruza 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero, Yehova anamuyang’ana ndi kunena kuti: “Pita ndi mphamvu zimene ndakupatsazi,+ ndipo udzapulumutsadi Isiraeli m’manja mwa Amidiyani.+ Si ine amene ndakutuma kodi?”+
14 Atatero, Yehova anamuyang’ana ndi kunena kuti: “Pita ndi mphamvu zimene ndakupatsazi,+ ndipo udzapulumutsadi Isiraeli m’manja mwa Amidiyani.+ Si ine amene ndakutuma kodi?”+