Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano Abulamu anayenda m’dzikomo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya More.+ Pa nthawiyo n’kuti m’dzikomo muli Akanani.

  • Genesis 33:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Patapita nthawi, Yakobo anafika bwinobwino kumzinda wa Sekemu,+ m’dziko la Kanani,+ akuchokera ku Padana-ramu.+ Atafika, anamanga msasa pafupi ndi mzindawo.

  • Yoswa 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya m’dera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, m’dera lamapiri la Yuda.

  • Oweruza 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu+ kwa abale a mayi ake. Kumeneko anayamba kulankhula nawo ndiponso kulankhula ndi banja lonse la bambo a mayi akewo kuti:

  • Machitidwe 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako mafupa awo anawatengera ku Sekemu,+ kumene anakawaika m’manda.+ Anawaika m’manda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori mu Sekemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena