Genesis 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Abulamu anayenda m’dzikomo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya More.+ Pa nthawiyo n’kuti m’dzikomo muli Akanani. Genesis 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita nthawi, Yakobo anafika bwinobwino kumzinda wa Sekemu,+ m’dziko la Kanani,+ akuchokera ku Padana-ramu.+ Atafika, anamanga msasa pafupi ndi mzindawo. Genesis 34:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana ena a Yakobo anamalizitsa amuna omwe anali atapwetekedwa koopsa, n’kutenga katundu yense wa mumzindamo. Anatero chifukwa anthuwo anagwiririra mlongo wawo.+ 1 Mafumu 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Rehobowamu+ anapita ku Sekemu,+ chifukwa kumeneko n’kumene Aisiraeli onse anasonkhana kuti akamulonge ufumu. Machitidwe 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako mafupa awo anawatengera ku Sekemu,+ kumene anakawaika m’manda.+ Anawaika m’manda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori mu Sekemu.+
6 Tsopano Abulamu anayenda m’dzikomo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya More.+ Pa nthawiyo n’kuti m’dzikomo muli Akanani.
18 Patapita nthawi, Yakobo anafika bwinobwino kumzinda wa Sekemu,+ m’dziko la Kanani,+ akuchokera ku Padana-ramu.+ Atafika, anamanga msasa pafupi ndi mzindawo.
27 Ana ena a Yakobo anamalizitsa amuna omwe anali atapwetekedwa koopsa, n’kutenga katundu yense wa mumzindamo. Anatero chifukwa anthuwo anagwiririra mlongo wawo.+
12 Rehobowamu+ anapita ku Sekemu,+ chifukwa kumeneko n’kumene Aisiraeli onse anasonkhana kuti akamulonge ufumu.
16 Kenako mafupa awo anawatengera ku Sekemu,+ kumene anakawaika m’manda.+ Anawaika m’manda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori mu Sekemu.+