Genesis 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Abulahamu anamveradi Efuroni, n’kumuyezera siliva wokwanira mtengo umene Efuroniyo ananena pamaso pa ana a Heti. Anamuyezera siliva wolemera masekeli 400, malinga ndi muyezo wovomerezeka ndi amalonda pa nthawiyo.+
16 Chotero Abulahamu anamveradi Efuroni, n’kumuyezera siliva wokwanira mtengo umene Efuroniyo ananena pamaso pa ana a Heti. Anamuyezera siliva wolemera masekeli 400, malinga ndi muyezo wovomerezeka ndi amalonda pa nthawiyo.+