Ezara 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno ndinawayezera siliva, golide ndi ziwiya.+ Zimenezi zinali zopereka za kunyumba ya Mulungu wathu zimene mfumu,+ aphungu ake,+ akalonga ake ndi Aisiraeli onse+ amene anali kumeneko anapereka. Machitidwe 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako mafupa awo anawatengera ku Sekemu,+ kumene anakawaika m’manda.+ Anawaika m’manda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori mu Sekemu.+
25 Ndiyeno ndinawayezera siliva, golide ndi ziwiya.+ Zimenezi zinali zopereka za kunyumba ya Mulungu wathu zimene mfumu,+ aphungu ake,+ akalonga ake ndi Aisiraeli onse+ amene anali kumeneko anapereka.
16 Kenako mafupa awo anawatengera ku Sekemu,+ kumene anakawaika m’manda.+ Anawaika m’manda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori mu Sekemu.+