Genesis 50:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anamunyamula n’kupita naye kudziko la Kanani. Kumeneko anakamuika m’phanga m’munda wa Makipela, woyang’anana ndi munda wa Mamure.+ Mundawo ndi umene Abulahamu anagula kwa Efuroni Mhiti, kuti akhale ndi manda.
13 Anamunyamula n’kupita naye kudziko la Kanani. Kumeneko anakamuika m’phanga m’munda wa Makipela, woyang’anana ndi munda wa Mamure.+ Mundawo ndi umene Abulahamu anagula kwa Efuroni Mhiti, kuti akhale ndi manda.