Ezara 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ziwiya+ zimene ukupatsidwa kuti zikagwiritsidwe ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wako, ukazipereke zonse ku Yerusalemu n’kukaziika pamaso pa Mulungu.+
19 Ziwiya+ zimene ukupatsidwa kuti zikagwiritsidwe ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wako, ukazipereke zonse ku Yerusalemu n’kukaziika pamaso pa Mulungu.+