Genesis 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa. Genesis 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Abulamu anayenda m’dzikomo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya More.+ Pa nthawiyo n’kuti m’dzikomo muli Akanani.
19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa.
6 Tsopano Abulamu anayenda m’dzikomo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya More.+ Pa nthawiyo n’kuti m’dzikomo muli Akanani.