Oweruza 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu kwa azichimwene awo a mayi ake. Ndipo anauza amalume akewo komanso banja lonse la bambo a mayi ake kuti:
9 Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu kwa azichimwene awo a mayi ake. Ndipo anauza amalume akewo komanso banja lonse la bambo a mayi ake kuti: