Oweruza 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu+ kwa abale a mayi ake. Kumeneko anayamba kulankhula nawo ndiponso kulankhula ndi banja lonse la bambo a mayi akewo kuti:
9 Patapita nthawi, Abimeleki+ mwana wa Yerubaala, anapita ku Sekemu+ kwa abale a mayi ake. Kumeneko anayamba kulankhula nawo ndiponso kulankhula ndi banja lonse la bambo a mayi akewo kuti: