Oweruza 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako atsogoleri onse a ku Sekemu ndi anthu onse a ku Beti-milo anasonkhana kumene kunali chipilala pafupi ndi mtengo waukulu ku Sekemu. Kumeneko anamuika Abimeleki kukhala mfumu.+
6 Kenako atsogoleri onse a ku Sekemu ndi anthu onse a ku Beti-milo anasonkhana kumene kunali chipilala pafupi ndi mtengo waukulu ku Sekemu. Kumeneko anamuika Abimeleki kukhala mfumu.+