Genesis 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho anthuwo anapereka kwa Yakobo milungu yachilendo+ yonse imene anali nayo, ndi ndolo* zimene anavala m’makutu. Kenako Yakobo anafotsera+ zinthuzo pansi pa mtengo waukulu pafupi ndi Sekemu. Yoswa 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Yoswa analemba mawu amenewa m’buku la chilamulo cha Mulungu.+ Atatero, anatenga mwala waukulu+ ndi kuuika pansi pa mtengo waukulu kwambiri+ umene uli pafupi ndi malo opatulika a Yehova.
4 Choncho anthuwo anapereka kwa Yakobo milungu yachilendo+ yonse imene anali nayo, ndi ndolo* zimene anavala m’makutu. Kenako Yakobo anafotsera+ zinthuzo pansi pa mtengo waukulu pafupi ndi Sekemu.
26 Ndiyeno Yoswa analemba mawu amenewa m’buku la chilamulo cha Mulungu.+ Atatero, anatenga mwala waukulu+ ndi kuuika pansi pa mtengo waukulu kwambiri+ umene uli pafupi ndi malo opatulika a Yehova.