Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+ Oweruza 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pakati pa anthu okhala ku Yabesi-giliyadi+ anapeza atsikana 400, anamwali+ amene anali asanagonepo ndi mwamuna. Amenewa anawabweretsa ku msasa ku Silo,+ m’dziko la Kanani.
18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+
12 Koma pakati pa anthu okhala ku Yabesi-giliyadi+ anapeza atsikana 400, anamwali+ amene anali asanagonepo ndi mwamuna. Amenewa anawabweretsa ku msasa ku Silo,+ m’dziko la Kanani.